Msonkhano wa mmaiko woimilira chigawo chakum’mwera kwa Africa pa nkhani
ya Ulimi mu Africa womwe umatchedwa KADIPI, wangotha kumene mdziko la Zambia. Mtola nkhani wathu Sydney Katunga Phiri anali nawo ku msonkhanowu ndipo watitumizira ripotili.

Chipani cha UPND ku Zambia chachotsa mamembala ake 15
07:02

Chiwonetselo cha za malonda cha International Trade Fair chikuchitika ku Malawi
06:23

Komiti ya nyumba ya malamulo ku Malawi yayamba kufufuza za imfa ya a Chilima
06:43