Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Komiti ya nyumba ya malamulo ku Malawi yayamba kufufuza za imfa ya a Chilima

View descriptionShare
 

Komiti yapadela ya nyumba ya malamulo ku Malawi yomwe inakhazikitsidwa ndi cholinga chofufuza za ngozi yomwe inapha yemwe anali wachiwiri kwa president Dr Saulosi Chilima ndi anthu ena asanu ndi atuta yayamba kupanga wa ngoziyi. George Mhango wabwela ndi nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 978 clip(s)