Chipani cholamula boma m’dziko la Zambia cha United Party for National Development , chachotsa pakati pake mamembala 15 omwe akuti adachita chipongwe kwa membala wa chipanichi yemwe wasankha kuyima payekha pa udindo wa uphungu ku Mazabuka. Yemwe adachitidwa chipongwechi ndi Gary Nkombo, yemwe kale anali nduna ya maboma ang’ono-ang’ono komanso phungu wa nyumba ya malamulo ku Mazabuka. Daniel Elisha Banda akulongosola.

Chiwonetselo cha za malonda cha International Trade Fair chikuchitika ku Malawi
06:23

Komiti ya nyumba ya malamulo ku Malawi yayamba kufufuza za imfa ya a Chilima
06:43

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46