Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mpungwe pungwe wabuka mchipani chotsutsa boma ku Malawi cha MCP

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
814 clip(s)
Loading playlist

Mpungwepungwe wabuka mchipani chotsutsa boma cha Malawi Congress Party--MCP  mdziko la Malawi pomwe kagulu kena kakufuna mtsogoleri wa Chipanichi  Dr Lazarus Chakwera kuti  atule pansi udindo wawo pomwe ena akuti kaguluko kangotumidwa chabe. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 957 clip(s)