Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mphekesela ikuti Bungwe la masankho ku Zambia la ECZ likufuna kusintha malamulo

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
803 clip(s)
Loading playlist

Pakumveka manong'onong'o akuti bungwe lomwe limayendetsa zisankho mdziko la Zambia la Electoral Commission of Zambia, ECZ,  likufuna kusintha mfundo zina za  malamulo oyendetsera zisankho. Nkhaniyi yabweretsa mantha pakati pa zipani zotsutsa boma. Poyamba Daniel Elisha Banda walankhulana ndi mkulu wa bungwe la Anti-Voter Apathy Project, AVAP, wa chigao cha Eastern Province, a Maumba Ngoma.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 946 clip(s)