Mafuta a galimoto ndi ndege akwera kwambiri mdziko la Malawi zomwe zikupereka chiopsezo kuti mwina zinthu zofunikila pamoyo wa anthu zikwera mtengo. Mafuta a petrol akwera ndi 34 % kufika pa K6,672 kuchoka pa K4,935 ndipo Dizilo wakwela ndi 35% kufika pa mtengo wa K6,687 kuchoka pa K4,945 . Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse

Mabungwe ena ku Malawi adzudzula zomwe Alexious Kamangila akulankhula
07:45

A katswili andale ena ku Malawi ati a Chakwera sanalankhule bwino pa maliro
06:45

Mtsogoleri wa South Sudan Salva Kiir wachotsa sipikala wa nyumba ya Malamulo
05:50