Mabungwe omenyela ma ufulu a anthu mdziko la Malawi a MABLEM ndi HRCC adzudzula mchitidwe ogwilitsa ntchito masamba amchezo molakwikika pamene loya wina Alexious Kamangila akutchula akulu akulu ena kuti akuchita za katangale . Jayne Chilimampunga wabwela ndi nkhani yonse

A katswili andale ena ku Malawi ati a Chakwera sanalankhule bwino pa maliro
06:45

Mtsogoleri wa South Sudan Salva Kiir wachotsa sipikala wa nyumba ya Malamulo
05:50

Mchitidwe wa anthu otengela lamulo m’manja wakula ku Zambia
06:26