Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

A katswili andale ena ku Malawi ati a Chakwera sanalankhule bwino pa maliro

View descriptionShare
 

Zomwe anayankhula mtsogoleri wakale wa dziko la Malawi Dr Lazarus Chakwera  kuti anthu asamutengere ku mtoso ndi munthu okonda mtendere zautsa zoyankhula zosiyana pakati pa Malawi. Mtolankhani mzathu mdziko la Malawi Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 964 clip(s)