Madera ambiri a dziko la Zambia akuyembekezeka kulandira mvula yochepa kwambiri komanso zokolola zochepa m’nyengo ya ulimi ya 2026/2027. Ichi ndi chifukwa cha nyengo ya El Nino yomwe idzakhudza madera ambiri adzikolo. Izi zapangitsa akatswiri azanyengo komanso unduna wa za ulimi kupempha alimi kuti alime mbewu zomwe zimacha msanga, pofuna kupewa njala. Daniel Elisha Banda akulongosola.

Boma la Zambia lasayina pangano la za umoyo ndi boma la USA la $2.49 biliyoni
06:43

Vuto la kusowa kwa mafuta agalimoto likupitilira ku Malawi
06:21

Boma la Zimbabwe liyendetsa maliro a mponda matiki Wicknell Chivayo
05:12