Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Vuto la kusowa kwa mafuta agalimoto likupitilira ku Malawi

View descriptionShare
 

Anthu ambiri mdziko la Malawi adzudzula bungwe lowona za mafuta ndi magetsi la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) ndi  bungwe lokhometsa msonkho la Malawi Revenue Authority (MRA)  polekelera ma venda kumagulitsa mafuta agalimoto pa msika osavomelezeka komanso okwera mtengo kwambiri pamene mafuta akusowa m’madera  mdzikolo. Jayne Chilimampunga wabwela ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,108 clip(s)