Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Boma la Zambia lasayina pangano la za umoyo ndi boma la USA la $2.49 biliyoni

View descriptionShare
 

 Boma la Zambia lasayina pangano la za umoyo ndi boma la United States of America  la ndalama zokwana 2.49 biliyoni US dollars ndipo unduna wa za umoyo wati ndalamazi  zithandizila kupititsa patsogolo ntchito za  umoyo mdziko la Zambia. Ziyenela Zimba akutambasula bwino nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,108 clip(s)