Msilikali wina wadziko la Uganda Lefutenanti Matanda Mabonga watulutsa makanema omwe akuonetsa anthu ena omwe amazuzidwa akagwidwa kunyumba zomwe asilikali adzikolo a UPDF anamanga pofuna kulangiramo anthu otsutsa boma zija pachingerezi amati ma safe house kapena torture chambers.Mtolankhani mzathu ku m’mawa kwa Africa Alfred Dzaoneni ali ndi zambiri.

Boma la Zambia lasayina pangano la za umoyo ndi boma la USA la $2.49 biliyoni
06:43

Vuto la kusowa kwa mafuta agalimoto likupitilira ku Malawi
06:21

Madera ambiri a dziko la Zambia akuyembekezeka kulandira mvula yochepa kwambiri
07:20