Nduna ya za chuma mdziko la Zambia Situmbeko Musotokwane, yalengeza kuti boma tsapano lidzilola Ochita malonda a za migodi kuti adzipereka misonkho kugwiritsira ndalama ya dziko la China kuphatikiza ya dziko America. Ziyenela Zimba akufotokoza zambiri

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55

Akatswili a ndale ati A Mutharika akutsogolera bwino Malawi
06:24