Bwalo la milandu lalikulu la dziko la South Africa layimitsa mwambo wakuika maliro mdzikolo a yemwe kale anali president wa Zambia, Edgar Chagwa Lungu. A Lungu anamwalira pa 5 June 2025 pa chipatala cha Medclinic Medforum mu mzinda wa Pretoria. Asanamwalire, a Lungu anasiya mau ku banja lao akuti president Hakainde Hichilema asakapezeke pa maliro awo. Daniel Elisha Banda ali ndi nkhaniyi.

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53