Mu mzinda wa Lusaka, nzika za Zambia lero zinasonkhana kukumbukira tsiku lobadwa komanso mbiri ya mtsogoleri oyamba wa dzikolo Kenneth Kaunda. Atsogoleri a boma, andale, atsogoleri a mipingo komanso akazembe a mayiko osiyanasiyana anasonkhana ku kachisi wa Cathedral of the Holy Cross komwe kwachitikira mapemphero ndi chikumbutso cha tsiku lofunika ili.Daniel Elisha Banda ali ndi tsatanetsatane wa nkhaniyi

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25