Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Dziko la Zambia lakondwelera mtsogoleri oyamba Kenneth Kaunda

View descriptionShare
 

Mu mzinda wa Lusaka, nzika za Zambia lero zinasonkhana kukumbukira tsiku lobadwa komanso mbiri ya mtsogoleri oyamba wa dzikolo Kenneth Kaunda. Atsogoleri a boma, andale, atsogoleri a mipingo komanso akazembe a mayiko osiyanasiyana anasonkhana  ku kachisi wa  Cathedral of the Holy Cross komwe kwachitikira mapemphero ndi chikumbutso cha tsiku lofunika ili.Daniel Elisha Banda ali ndi tsatanetsatane wa nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)