Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Chiwelengelo cha anthu odzipha mdziko la Malawi chikuchulukila

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
503 clip(s)
Loading playlist

Chiwelengelo cha anthu odzipha chikupitilira kukwela  mdziko la Malawi Pamene anthu 256 anadzipha kuyambila  m'mwezi wa January kufikila mwezi wa June Chaka chino chomwe ndi chokwela kuposela chaka chatha mnyengo ngati yomweyi, ndipo ambiri mwa anthu odzipha ndi abambo omwe akufika pa chiwelengelo cha 226 pamene chiwelengo cha amayi chili pa 30.

George Mhango wabwela ndi nkhani yonse.

 

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)