Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Mtsogoleri wa Zambia wachotsa atsogoleri a bungwe lothana ndi katangale

View descriptionShare

Mtsogoleri wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema wachotsa ntchito atsogoleri  omwe anali mu bungwe lomwe limayang'anira chigao cha Anti-Corruption Commission chomwe chimalimbana ndi ziphupu komanso katangale  mdzikolo . Mkulu wa bungwe la achinyamata la Youth Development Foundation, Muyeye Chinoya , wati chiganizo cha President Hichilema pa nkhaniyi chilibwino. Daniel Elisha Banda ali wadza ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)