Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu ena ku Zambia adzudzula president Hichilema posintha nduna ya za umoyo

View descriptionShare

Mankhwala aboma la Zambia pa muyeso wa 65 million US dollars apezeka ku nkhokwe yosunga katundu yomwe ili mmanja mwa anthu wamba ,Mwa  ichi, President Hakainde Hichilema wachotsa nduna ya za umoyo ,Sylvia Masebo, ndikuipereka  ku unduna wa za nthaka.

Anthu wamba ndi akuluakulu ena azipani zotsutsa adzudzula ganizo la President Hichilema.

Daniel Elisha Banda wadza ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    503 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 640 clip(s)