Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Bungwe la MERA ku Malawi lakweza gasi ndi 19.65%

View descriptionShare

Bungwe lowona za mafuta mdziko la Malawi la Malawi Energy Regulatory Authority MERA, lakweza mtengo wa gasi ndi 19.65 pelecenti  kuchoka pa K3,740 kufika pa K4,475.00 pa kilogram imodzi ndipo bungweli lati mafuta a galimoto a Petrol ndi diesel saakwera mtengo. George Mhango akufotokoza zambiri.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 957 clip(s)