Bungwe lomwe limagula mbewu kwa alimi mdziko la Zambia la Food Reserve Agency, FRA, lalengeza kuti chaka chino lidzagula chimanga pa thumba limodzi la 50 KG pa mtengo wa K340. Koma chaka chatha mtengo wa thumbali unali pa mtengo wa K330. Nkhaniyi yalandilidwa ndi maganizo wogawikana pakati pa alimi. Daniel Elisha Banda ali ndi nkhaniyi.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11