Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Bungwe la CDEDI ku Malawi lidzachititsa zionetselo pa 21 November 

View descriptionShare

Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives laitana zipani zonse zotsutsa boma kuti zidzatenge nawo gawo pa zionetsero zikudzachitika la chinai pa 21 November 2024 pomwe akukakamiza wa pa mpando wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority komanso nduna ya Mphamvu za magetsi ndi mafuta kutula pansi udindo ponena kuti alephera ntchito yawo chifukwa tsopano mavuto akusowa kwa mafuta akutha miyezi itatu mdziko la Malawi.

Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)