Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

M’modzi mwa alimi ku Malawi Victoria Mafulirwa walimbikitsa amayi amalonda

View descriptionShare

Mayi Victoria Mafulirwa yemwe ndi mulimi wamkulu mdziko la Malawi, walimbikitsa amayi kuti apite patsogolo pa chuma ku msonkhano othandiza amayi kuchita bwino pa chuma  kudzela mu ma business  ku msonkhano omwe ukuchitika mu mzinda wa johannesburg mdziko la south Africa otchedwa Women Creating Wealth. Stella Longwe walankhula ndi mayiwa  

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)