Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

A Dalitso Kabambe awasankha kukhala president wa UTM ku Malawi

View descriptionShare

Governor  wakale wa bank yaikulu mdziko la Malawi ya Reserve, a Dr Dalitso Kabambe  awasankha kukhala mtsogoleri wachipani cha Chachikulu chotsotusa boma mdziko cha United Transformation  Movement  --UTM pa msonkhano osankha adindo a mchipanichi omwe unachitika dzulo pa 17 November 2024, a Kabambe ati iwo akadzasankhidwa kukhala mtsogoleri  wadzikolo adzathetsa umphawi,katangale komanso kusalana mitundu. Kondwani Nyamasauka ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)