Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu mdziko la Malawi la Anti Corruption Bureau - ACB, lamanga mkulu wakale wa asilikali a nkhondo General Paul Valentino Phiri pomuganizira pa milandu isanu yokhudza kugwiritsa ntchito udindo wake molakwika komanso kugwiritsa ntchito katundu opezeka mu njira zosavomelezeka. George Mhango ali ndi nkhani yonse

Boma la Zambia lasayina pangano la za umoyo ndi boma la USA la $2.49 biliyoni
06:43

Vuto la kusowa kwa mafuta agalimoto likupitilira ku Malawi
06:21

Madera ambiri a dziko la Zambia akuyembekezeka kulandira mvula yochepa kwambiri
07:20