Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Brian Mundubile ndi Makebi Zulu a Tonse Alliance ku Zambia awonekela ku khothi

View descriptionShare
 

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
965 clip(s)
Loading playlist

Mtsogoleri wa mgwilizano osutsa boma wa Tonse Alliance Pamodzi mdziko la Zambia Brian Mundubile ndi wachiwiri wake Makebi Zulu lero anawonekela ku bwalo la milandu  m’boma la Solowezi ndipo khothi lakana pempho la akulu akuluwa lofuna kupeleka umboni wa pakamwa pa mlandu omwe akuzengedwa ochita zokopa anthu kuti awukile dzikolo. Ziyenela Zimba akufotokoza zonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 1,108 clip(s)