Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Boma la Zimbabwe layimitsa kugulitsa miyila ya mtengo wapatali kunja

View descriptionShare

Boma la Zimbabwe  lalengeza kuti kugulitsa miyala ya mtengo wa patali kuyimitsidwe kufikila mtsogolo chifukwa chokuti miyala imagulitsidwa osasulidwa zomwe zimapangitsa kuti miyala izigulitsidwa motsika mtengo. John Kassim akulongosola

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 957 clip(s)