Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Boma la Zambia lasiya kuletsa Julius Malema wa EFF kulowa mdzikolo

View descriptionShare

Boma la Zambia lachotsa chiletso cha zaka zisanu ndi ziwiri chomwe chimaletsa mkulu wa chipani chotsutsa cha EFF cha mdziko la South Africa, Julius Malema, kukacheza ku dziko la Zambia. Yemwe kale anali President wa dziko la  Zambia,  Edgar Chagwa Lungu anapereka chiletso chimenechi mu chaka cha 2017 pambuyo pa kudzudzulidwa ndi  Malema kamba kakuti a Lungu  ankapondereza ma ufulu a atsogoleri azipani zotsutsa.  Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. Zochitika (Chinyanja)

    556 clip(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 695 clip(s)