Nthambi ya thangatani ana ya UNICEF ya m’bungwe la United Nations yati atsikana ochepela zaka 18 zakubadwa ofika pafupi fupi 1.8 miliyoni amakwatila mdziko la Zambia. Ziyenela Zimba akufotokoza zambiri.

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55

Akatswili a ndale ati A Mutharika akutsogolera bwino Malawi
06:24