Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Atsikana 1.8miliyoni amakwatila ali ang’ono ku Zambia

View descriptionShare

Nthambi ya thangatani ana ya UNICEF ya m’bungwe la United Nations yati atsikana ochepela zaka 18 zakubadwa  ofika pafupi fupi 1.8 miliyoni amakwatila mdziko la Zambia. Ziyenela Zimba akufotokoza zambiri.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 927 clip(s)