Pali manong’o-non’go akuti aphungu achipani chotsutsa boma cha Patriotic Front, PF, mdziko la Zambia amene anavotela Bill 7 akumaopsyezedwa ndi anthu osadziwika bwino kuti adzaphedwa. M’modzi mwa akuluakulu achipanichi, Philip Bobat Phiri wati nkhani ya ziopsyezo ndi yoipa komabe aphungu achipani chake anachita bwino kuvotela Bill 7. Daniel Elisha Banda akusimba.

Tonse Alliance ku Zambia yawina masankho a dela Chawama
07:32

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55