Boma la Zambia lakhazikitsa lamulo latsopano lomwe likuchotsa belo kwa anthu opalamula milandu yogwilira amai, atsikana komanso kuchita za chiwele wele pa chibale. Lamuloli lidzayamba kugwira ntchito mwezi uno wa April, ndipo likuyembekezeka kuthandiza kuchepetsa nkhanza zogwilira mdzikolo. Daniel Elisha Banda akusimba

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25