Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu opezeka ndi mlandu ogwilira samapatsidwa belo ku Zambia

View descriptionShare
 

Boma la Zambia lakhazikitsa lamulo latsopano lomwe likuchotsa belo kwa anthu opalamula milandu yogwilira amai, atsikana komanso kuchita za chiwele wele pa chibale. Lamuloli lidzayamba kugwira ntchito mwezi uno wa April, ndipo likuyembekezeka kuthandiza kuchepetsa nkhanza zogwilira mdzikolo. Daniel Elisha Banda akusimba

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 975 clip(s)