Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu ndi Mabungwe ku Malawi atsutsa za ripoti ya kumangidwa kwa Martha Chizuma

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
814 clip(s)
Loading playlist

Kusowa kwa ena mwa mapepala(Documents) mu ripoti lokhudza kumangidwa kwa nkulu wa bungwe lothana ndi ziphuphu ndi katangale mdziko la Malawi mai Martha Chizuma, kwadzutsa Mapiri pachigwa.

A Malawi ambiri pamodzi ndi mabungwe ena sakukondwa ndi zomwe zatulutsidwazi .Mntsogoleri wa dzikoli Rev. Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, adakhazikitsa gulu la anthu khumi ndi mmodzi(11) kuti afufuze za kumangidwa kwa mai Chizuma, yemwe patsikulo ankayenera kukaonana ndi mntsogoleri wadzikolo.

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 957 clip(s)