Mwambo oyika m’manda thupi la mtsogoleri wakale wa Zambia, Edgar Lungu unayamba ndi mapemphelo pa tchalitchi cha Cathedral of the Christ the King, m’dela la Hillbrow, mu mzinda wa Johannesburg ku South Africa koma siwunapitilire chifukwa cha chigamulo cha khothi la mdzikolo choletsa kuyika maliro, ndipo Channel Africa yayankhula ndi lawyer wa banja la Malemu a Lungu, Makebi Zulu, bambo Devin Mubhanga ochokela ku dziko la Zambia ndi bambo Lebogang Moepeng mkulu wa chipani chotsutsa cha MK mdziko la South Africa

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11