Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Anthu ambiri Ku Malawi akufuna pakhale lamulo loti opha nzake aziphedwa

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
803 clip(s)
Loading playlist

Anthu ambiri akufuna kuti boma likhazikitse lamulo loti opha nzake naye aziphedwa, ndikuti president azisainira.

Izi zadza pamene mchitidwe ophana chisawawa ukunka nuchulukira ku Malawi. Sabata yatha ku Mwanza anthu anapeza mafupa a ana aakazi  awiri wina zaka 10 wina 12 mminda yosiyana, atasowa kwa masiku ambiri. Jayne Chilimampunga wadza ndi nkhaniyi

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 946 clip(s)