Makampani ambiri ogula mbewu ya fodya mdziko la Zambia alengeza mitengo ya chigawo cha ulimi wa 2025/2026. Mitengo ya chaka chino ili pakati pa 40 cents ndi 5 dollars-20 cents pa kg imodzi ndalama ya dziko la America . Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse.

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

AIPAC ku Zambia yatsuta kuwunika ma bilu pomwe paliyamenti itseke pa 15 May 2026
10:17

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25