Zochitika (Chinyanja)Zochitika (Chinyanja)

Alimi ku Malawi ayambanso kugulitsa chimanga ku NFRA

View descriptionShare

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
803 clip(s)
Loading playlist

Boma la Malawi kudzela mu bungwe lowona za chakudya la National Food Reserve Agency NFRA, layambanso kugula chimanga kwa alimi pamene linasiya kugula chimanga masiku apitawo chifukwa chokuti ndalama zogulira zinatha. George Mhango wabwela ndi nkhani yonse .

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Zochitika (Chinyanja)

Current Affairs featuring various segments. 
Recent clips
Browse 946 clip(s)