Akatswiri andale mdziko la Malawi ati zomwe walankhula mntsogoleri wakale wa dzikolo Prof. Author Mutharika, ndi zosathandiza ku chitukuko cha dzikolo.
A Mutharika omwenso ndi mntsogoleri wa chipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP) anachititsa mnsonkhano kumapeto kwa sabatayi, komwe mwa zina ati President wa dziko lino Rev. Dr. Lazarus McCarthy Chakwera atule pansi udindo wawo chifukwa cha kukwela mtengo kwa katundu komanso kuchuluka kwa katangale.

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11