Akatswili osiyana siyana a mdziko la Malawi, alankhulapo pa za mtsogoleri wa dzikolo professor Arthur Peter Mutharika, kukwanitsa masiku 100 chiyambileni kulamula pambuyo popambana masankho chaka chatha. George Mhango akusimba.

Anthu a chi alubino akupitilira kuchitidwa nkhanza ku Malawi
07:17

Alimi ena ku Zambia akudikilabe boma liwapatse malipiro atagulitsa mbewu ku FRA
07:55

MICHAEL CHANG AKUFUNA KUTI ATULUTSIDWE MNDENDE KU AMERICA
08:31