Bungwe lodziyimira palokha m’dziko la Zambia la Action for Policy Analysis Centre, AIPAC, ladzudzula nyumba ya malamulo chifukwa chofuna kuwunika ma bilu oposa 70 pomwe kwatsala masiku atatu okha kuti itsekedwe. Mkulu wa bungweli, Solomon Ngoma, akuti ntchito yopanga malamulo ndi yofunika koma ikuchitika pa nthawi yosayenera chifukwa aphungu ambiri sakumapezeka pa zokambirana zofunika. Daniel Elisha Banda akutambasula nkhaniyi.

Venancio Mondlane wati anthu alile maliro a Anselmo Vicente ku Mozambique
05:46

Anthu 7 aphedwa ku Malawi pogawaganizila kuti akusowetsa maliseche
05:25

Bungwe la CHREA ku Malawi likufuna kuti akaidi azichita za dama ndi akazi awo
07:53