Zigao zonse khumi za dziko la Zambia lero zachita chisangalalo cha achinyamata cha Youth Day ndipo chapmutu cha chaka chino chili motere: Dzukani ndi Kuuluka . Koma chisangalalo chachikulu cha dziko lonse chayendetsedwa ndi President Hakainde Hichilema mu boma la Solwezi ku chigao cha North-western Province. Daniel Elisha Banda ali ndi nkhani yonse

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53