Anthu ambiri mdziko la Malawi apempha bungwe lothana ndi katangale la ACB kuti afufuze za mchitidwe wa katangale ku nthambi ya polisi pamene apolisi akumapempha ndalama kwa anthu kuti achite ntchito yawo.Jayne Chilimampunga wabwela ndi nkhani yonse

Nyumba ya malamulo ku Malawi yakhazikitsa komiti yofufuza imfa ya a Chilima
08:07

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11