Anthu anayi omwe anamangidwa mdziko la Malawi kapena kuti akaidi a mndende zamdzikolo awasankhila msukulu zaukanjede zosiyanasiyana ndipo iwo awaturutsa kuti akapitilize maphunziro awo, izi zasangalatsa akatswiri omenyera ufulu.
Kondwani Nyamasauka wacheza ndi Amos Chibwana katswiri omenyera ufulu wa anthu mdziko la Malawi.

Mtsogoleri wachipani chotsutsa cha NUP ku Uganda Bobi Wine watuluka mdzikolo
06:12

Achinyamata ku Zambia ati achinyamata apatsidwe mwayi otukula miyoyo yawo
09:11

Mchitidwe wa uchifwamba ukuchulukila ku Malawi
06:53