News in ChinyanjaNews in Chinyanja

MABUNGWE A MISA NDI DVV AKUPHUNZITSA ATOLA NKHANI ZA MASUKULU A KWACHA KU MALAWI

View descriptionShare

News in Chinyanja

A news and current affairs show produced live by the current affairs team.
1,423 clip(s)
Loading playlist
CHINYANJA: Nthambi yoyang’anila atola nkhani ya Media International of Southern Africa Malawi mogwirizana ndi nthambi ya Germany Adult Education Association akuphunzitsa atola nkhani ku dziko la Malawi pa nkhani ya kufalitsa kwa nkhani zokhuzana ndi ma sukulu ophuzitsa anthu achikulire za kwacha kapena kuti Adult learning and education.

ENGLISH: Media international of southern Africa in conjunction with DVV are conducting journalism courses to equip and empower Malawi journalists with reporting skills about adult education and literature.
  • Facebook
  • Twitter
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

  1. News in Chinyanja

    1,423 clip(s)

News in Chinyanja

A news and current affairs show produced live by the current affairs team.
Social links
Recent clips
Browse 2,102 clip(s)