MALAWI REVENUE AUTHORITY YAKHAZIKITSA NJIRA ZATSOPANO ZOTHANA NDI OTHAWA NSONKHO
CHINYANJA: Bungwe lotolela msonkho ku Malawi la Malawi revenue authority lathazikitsa ndondomeko zatsopano zofuna kuthetsa ntchitidwe ozemba kupeleka msonkho. ENGLISH: Malawi revenue authority has introduced new measures to deal with tax evaders.
ZAMBIA IDAKALIRA INFA YA MTSOGOLERI WAKALE KENNETH KAUNDA
CHINYANJA: Nzika za dziko la Zambia zidakalira infa ya mtsogoleri wakale Dr Kenneth Kaunda yemwe anamwalira pa 17 June chaka chimenechi mu nzinda wa Lusaka. ENGLISH: Zambians are still mourning the death of former leader Dr Kenneth Kaunda who passed away on the 17th June 2021 in Lusaka.
MABUNGWE A MISA NDI DVV AKUPHUNZITSA ATOLA NKHANI ZA MASUKULU A KWACHA KU MALAWI
CHINYANJA: Nthambi yoyang’anila atola nkhani ya Media International of Southern Africa Malawi mogwirizana ndi nthambi ya Germany Adult Education Association akuphunzitsa atola nkhani ku dziko la Malawi pa nkhani ya kufalitsa kwa nkhani zokhuzana ndi ma sukulu ophuzitsa anthu achikulire za kwacha ka…
PALI CHIOPHYEZO CHOKUTI ZIMBABWE IKHALA PA M’BINDIKILO OKHWIMA NDI KUKWELA KWA COVID-19
CHINYANJA: Pali chiophyezo chokuti dziko la Zimbabwe likhazikitsa m’bindikilo okhwima kaamba kakuti chiwelengelo cha matenda a Covid -19 chikukwela kwambili mumadera ena mdzikolo. ENGLISH: There are fears that the Zimbabwean government might impose strict lockdown measures due to rising numbers o…
MUUNI WA ZA MAPHUNZIRO
CHINYANJA: Pulogalamu younika za mavuto a za maphunziro mu Africa. ENGLISH: A programme that deals with education challenges and issues affecting the African society.
MABUNGWE OMENYELA UFULU KU ZAMBIA ACHITA ZIONETSERO KUTI BOMA LALOLEZA MIGODI KU NATIONAL PARK
CHINYANJA: Mabungwe aza chilengedwe ku Zambia akuchita zionetsero Kamba koti boma laloleza kampani ya Mwembe Shire resources kuti iyambe ntchito yokumba migodi ku nkhalango ya Lower Zambezi National Park ENGLISH: More than 30 civil society organisations have petitioned government for allowing an in…
CHIPATA PRESS CLUB YAPEMPHA NYUMBA ZOFALITSA NKHANI KUTI ZITETEZE ATOLA
CHINYANJA: Bungwe loyang’anila atola nkhani la chigawo cha ku mmawa mdziko Zambia la Chipata Press Club lapempha nyumba zofalitsa nkhani kuti ziteteze atola nkhani awo ku matenda a Covid-19 powapatsa zipangizo zofunikira zozitchinjiriza ku matendawa. ENGLISH: Chipata Press Club has appealed to med…
ANTHU OZISINTHA KUKHALA AMUNA KAPENA AKAZI LGBTIQ ANACHITA ZIWONETSERO KU MALAWI
CHINYANJA: Anthu ozisintha kukhala amuna kapena akazi mdziko la Malawi anachita ziwonetsero za kusalidwa poyenda ndawala yokapereka chikalata cha madandaulo ku ma office a khonsolo ya mu nzinda wa Lilongwe kuti apatsidwe chilolezo chomakwatilana ENGLISH: Lesbian, Gays, Bisexual, Transgender, Inter…
BOMA LA MOZAMBIQUE LAGWIRA ANTHU OMWE ANALOWA MDZIKOLO POPANDA CHILOLEZO
CHINYANJA: Apolisi mdziko la Mozambique agwila anthu olowa mdzikolo opanda chilolezo ENGLISH: Police in Mozambique have arrested dozens of illegal migrants.
MUUNI WA ZA UMOYO
CHINYANJA: Matenda a covid 19 akupitilira kugwila anthu ambiri mdziko la Zambia ENGLISH: Zambia experiences a surge in covid 19 infections.