Boma la Malawi layamba ntchito yosamutsa njobvu zokwana 250 komanso nyama zina ndi zina kuchokera ku Liwonde National Park kupita ku Kasungu National Park, komwe ndi malire ndi dziko la Zambia.
Mtolankhani wathu George Mhango walankhula ndi Bright Kumchedwa yemwe mkulu wa bungwe loyang’anira malo osungira nyama zakutchire pa ntchitoyi.

MUUNI WA ZA LUSO LA MAKONO NDI DANIEL BANDA
08:53

BUNGWE LA UNITED PURPOSE KU MOZAMBIQUE LIKHAZIKITSA MALO OTUNGIRA MADZI A UKHONDO
05:56

ANTHU ASANU AGAMULIDWA KUTI AKHALE MDENDE MOYO WAWO ONSE KU MALAWI
06:11