Oyimba wa ku Malawi amene akukhala mdziko la South Africa,Master Manda, waonetsa kuti khama limapindula pamene anayamba kuyimba ndi zida za lokolo zopanda magetsi ndipo pano amayimba ndi zida za magetsi. Iye akuyembekezeka kutulutsa chimbale masiku akubwelawa.