Katswili wa ndakatulo wa mdziko la Malawi amene akukhala mdziko la South Africa walemba ndakatulo yolira yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Malawi Dr Saulosi Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu amene anamwalira pangozi ya ndege masiku apitawo.