Malonje (Chinyanja)Malonje (Chinyanja)

Mozambique,Tanzania ndi Malawi, akhazikitsa nthambi ya Rovuma River Basin

View descriptionShare
 

Mayiko a Mozambique, Tanzania ndi Malawi, amaliza ntchito yokhazikitsa nthambi ya Rovuma River Basin yomwe iziyendetsa ndondomeko zakagwilitsidwe ntchito ka mitsinje ndi  nyanja zomwe mayikowa amagawana. Bright Sonjela ali ndi nkhani yonse

  • Facebook
  • X (Twitter)
  • WhatsApp
  • Email
  • Download

In 1 playlist(s)

Malonje (Chinyanja)

Upbeat music, interviewing artists interactive; have weekly feature on community members giving back 
Recent clips
Browse 60 clip(s)